ZAMBIRI ZOWAWA ZA MOYO WA SAULOS CHILIMA 1973-2024 ''Arafat Hamdan''
Hanifa Mw
0:00 / 0:00
ZAMBIRI ZOWAWA ZA MOYO WA SAULOS CHILIMA 1973-2024 ''Arafat Hamdan''
76 920 просмотров · 3 г. назад
Hanifa Mw
85,4 тыс. подписчиков
76 920 просмотров · 3 г. назад
SAULOS CHILIMA
Mu chaka cha 2018, pa nthawi yomwe Dr Saulos Chilima analengeza kutuluka kwawo ku chipani cha DPP ndikuyambitsa chawo cha United Transformational Movement (UTM), kunayamba kumnveka mphekesera zambiri zokhuza makolo awachiwiri kwa mtsogoleriyu. Anthu ena, makamaka odana nawo kamba kotuluka chipani cha DPP, anayamba kumafalitsa ma uthenga akuti dzina lawo si Saulos Chilima ndipo dzinali anachita kusintha atakula kale popeza dzina lawo lakubadwa ndi Arafat Hamdan. Izi zinali paliponse koma zinazizira popeza eniwa sanyankhe chilichonse.