ZACHIKONDI by Young JiGA (official Music Video)
William Kudambo
0:00 / 0:00
ZACHIKONDI by Young JiGA (official Music Video)
45 просмотров · 6 дн. назад
William Kudambo
8 подписчиков
45 просмотров · 6 дн. назад
Young JiGA, ndi Nyamata yemwe adachokera ku Mzuzu ndikudzakhazikika ku Lilongwe...
Ndipo amatha kuyimba komaso kuvina choncho chinali chapafupi kuti tikwanitse kujambula kanema ameneyi mosavuta.
Kwa ife tikupempha kwa nonse amene mungawonere kanema ameneyi ndikutiuza ma ganizo anu chofunika ndi support yanu kuti tipitirize ukupatsirani zokoma
Uyu ndikanema oyamba mu career yanga yojambula ngati muli ma mistake mutiuza.
Malo omwe tikupezekera ndi Mlezi village (Lilongwe, Lumbadzi, T/A Chitukula)
mukafuna kudziwa zambiri chonde tumani uthenga ku WhatsApp +265996132838.
Tagwiritsa ntchito SUNO AI maka ku mbali ya Audio production...
#makosa #minivlog #hype #hyyy #malayalam #malawi #viral #viralvideo #youtubeshorts #viralvideo