Utatu ndi Khristu | Ahnsahnghong
World Mission Society Church of God / Global
0:00 / 0:00
Utatu ndi Khristu | Ahnsahnghong
821 просмотр · 3 года назад
World Mission Society Church of God / Global
142 тыс. подписчиков
821 просмотр · 3 года назад
Mpingo wa Mulungu Umakhulupirira mwa
Mulungu Yehova, Yesu, ndi Khristu Ahnsahnghong
Awo amene amamvetsetsa Utatu angakhulupirire
ndi kuzindikira kuti zimene Mulungu Yehova
anachita zinachitidwa ndi Yesu, ndipo zimene
Yesu anachita zinachitidwa ndi Dzina
Latsopano loti Khristu Ahnsahnghong.
Athanso kumvetsetsa kuti mu badwo
wa Mzimu Woyera, Khristu Ahnsahnghong
ayenera kubwera ndi Mulungu Amayi, Mkwatibwi
wa Mzimu Woyera ndi kutsogolera anthu ku
chipulumutso kudzera mu Paska wa pangano latsopano.
Yesaya 43:11
Ine, Inetu ndine Yehova; ndipo
palibe Mpulumutsi, koma Ine ndekha.
Machitidwe 4:11-12
Iye ndiye . . .
Ndipo palibe chipulumutso mwa wina
yense, pakuti palibe dzina lina pansi pa
thambo la kumwamba, lopatsidwa mwa anthu,
limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
[Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.]
〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org
〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny
〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com