Перейти к содержимому

LUNTHA TV || CHIDZULO || 26 OCTOBER 2026

Luntha TV official

0:00 / 0:00

LUNTHA TV || CHIDZULO || 26 OCTOBER 2026

3 382 просмотра · Трансляция закончилась 1 день назад
Luntha TV official
29,7 тыс. подписчиков
3 382 просмотра · Трансляция закончилась 1 день назад
LUNTHA TV || CHIDZULO, TOPIC:Atangomaliza kudzudzula mchitidwe wa anthu ena omwe akuti aphwanya ina mwa galimoto zomwe zinapelekeza Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera kuchikondwelero cha mpingo wa CCAP, Ku Blantyre Synod dzulo, a Chakwera avomeleza kuti anthu ena akhala akuwanamiza pomwe anali m'boma ndipo atsindika Kuti izi sizidzachitikanso potengera ndi masomphenya awo odzalamuliranso dziko lino ngakhale ena nchipanichi akuwatukwana.Mukuzitsatira motani nkhanizi, nanga ndemanga yanu ndiyotani aMalawi ? || 26 OCTOBER 2026