SIKUCHIMWITSITSA
Philadelphia Singers
0:00 / 0:00
SIKUCHIMWITSITSA
4 925 просмотров · 1 мес. назад
Philadelphia Singers
5,41 тыс. подписчиков
4 925 просмотров · 1 мес. назад
Kukhala ndi ulumali, mavuto ambiri kapena kusayenda kwa zinthu si chifukwa cha machimo ayi. Ndi njira yomwe Mulungu amagwiritsa ntchito kuti aonetse ukulu wake panu pamene zinthu zikasintha. Izi ndi nyimbo yokhudza chiyembekezo ndi mphamvu ya Mulungu pa moyo wathu.
Having challenges, setbacks, or delays in life is not always because of sin. Sometimes God allows these moments to reveal His greatness when things finally change. This song is about hope and the power of God in our lives.