EYE WITNESS KUFOTOKOZA MOMWE ZINAKHALIRA KWA CHADZUNDA ON NUSTRAT OSMAN ABDUCTION
AM TV MALAWI
0:00 / 0:00
EYE WITNESS KUFOTOKOZA MOMWE ZINAKHALIRA KWA CHADZUNDA ON NUSTRAT OSMAN ABDUCTION
684 просмотра · 3 ч назад
AM TV MALAWI
210 тыс. подписчиков
684 просмотра · 3 ч назад
Mfumu Malinga 2 yaku Mingale kwa mfumu yayikulu Nsomba m'boma la Blantyre yati anthu ake akukhala ndi mantha kutsatira zimene zinachitika Lachinayi madzulo, apolisi ataomberana ndi zigawenga zimene zimasunga mokakamiza mzika ya ku Britain, a Nustrat Osman.
M'modzi mwa anthu amene anaona izi zikuchitika, a William Chimangeni, anati panachikita zinthu ngati akuonera kanema pakuti panali kusintha kwa zipolopolo komanso kithamangitsana.
A Chimangeni anati mwini wa kumpanda kumene kumachitika izi anali ochezeka ndipo anthu ozungulira malowa sanaganizire kuti angachite izi. Komabe, iwo apempha mafumu m'derali kuti adzimufufuza munthu bwinolomwe asanamugulitse malo.