Перейти к содержимому

#KING TWAIB JOHN MNDALA #CHIMBALANGA II AKULANDIRA MTSOGOLERI WOSANKHIDWA WA #PRESIDENT WA #MALAWI

KINGDOM OF WAYAO

0:00 / 0:00

#KING TWAIB JOHN MNDALA #CHIMBALANGA II AKULANDIRA MTSOGOLERI WOSANKHIDWA WA #PRESIDENT WA #MALAWI

396 просмотров · 1 год назад
KINGDOM OF WAYAO
171 подписчик
396 просмотров · 1 год назад
Kumufunila zabwino president wathu wstsopano Kulimbikitsa mafumu amtundu wa chiyao pogwila mchito limodzi ndi boma pothandiza kukweza chitukuko ndi maphumzilo komanso wulimi wamakono mdzikolathu lamalawi la mtendele Kutidziko lathu lizikhala ndichakudya chokwanila Chomwe chidziwafikila a Malawi wonse komanso kutsitsa kwamitengo yogulila zakudya ndizipangizo zamakono zawulimi Tiwaganizile amthu wokalamba Ana amasiye achinyamata womwe salipazimchito komanso amthu akundende kuti adzipeza zimthu zowayeneleza pa wumoyo watsiku nditsiku Boma komanso mabungwe ndi mafumu tigwilane manja pogwila mchito limodzi ndi boma la tsopano potukula ndi kukweza Malawi wstsopano Thank you Share with others