SHELIE Talks EP 5 | Kodi Maganizo a Achinyamata Amagwiritsidwa Ntchito? 🤔
Shelie Bello
0:00 / 0:00
SHELIE Talks EP 5 | Kodi Maganizo a Achinyamata Amagwiritsidwa Ntchito? 🤔
29 просмотров · 1 день назад
Shelie Bello
16 подписчиков
29 просмотров · 1 день назад
🎙️ SHELIE TALKS — EPISODE 5 ❤️✨
💭 KODI MAGANIZO A ACHINYAMATA AMAGWIRITSIDWA NTCHITO?
Kodi achinyamata amapatsidwa mpata wokwanira woti anene maganizo awo? Kapena nthawi zina maganizo awo amangonyalanyazidwa mpaka pamene akufunika kuti achite zinazake? 🤔
Mu episode iyi ya SHELIE Talks, tikukambirana za mmene maganizo a achinyamata amamvedwedwera komanso kufunika kopatsa achinyamata mwayi wofotokoza maganizo awo, kupanga zisankho komanso kutenga nawo mbali pa nkhani zomwe zimakhudza moyo wawo.
Kodi achinyamata amapatsidwa ulemu wokwanira? Kodi akuluakulu, atsogoleri komanso anthu ena amawamvetsera moona mtima? Kapena nthawi zina achinyamata amangokumbukiridwa pamene pakufunika thandizo lawo? 💭❤️
🎧 Onerani episode yonse ndipo tiuzeni maganizo anu mu comments!
💬 FUNSO LA EPISODEYI: Kodi mukuganiza kuti maganizo a achinyamata amamvedwa komanso kulemekezedwa mokwanira masiku ano? Fotokozani maganizo anu!
👍 Like
💬 Comment
📲 Share
🔔 Subscribe to SHELIE Talks for more interesting conversations about lifestyle and society.
Zikomo kwambiri chifukwa chothandizira SHELIE Talks! ❤️🫶🏽
🎙️ Podcast: SHELIE Talks
👩🏽💻 Host: Shelie Bello
🌍 Focus: Lifestyle & Society
#SHELIETalks #Episode5 #Achinyamata #MalingaliroAchinyamata #YouthVoices #MalawiPodcast #LifestyleAndSociety