Khalani Mboni Zanga ku Samariya ndi Kumalekezero a Dziko Lapansi | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
World Mission Society Church of God / Global
0:00 / 0:00
Khalani Mboni Zanga ku Samariya ndi Kumalekezero a Dziko Lapansi | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
652 просмотра · 3 г. назад
World Mission Society Church of God / Global
143 тыс. подписчиков
652 просмотра · 3 г. назад
Kuti Tiyende Mogwirizana ndi
Ulosiwu, Tiyenera Kudziwa Dzina
la Mzimu, ndi la Mkwatibwi.
Kuti tisunge mawu a
Mulungu akuti, “Khalani mboni
zolengeza za Mpulumutsi,” tiyenera
kudziŵa dzina la Yehova
m’badwo wa Atate, dzina
la Yesu m’badwo wa
Mwana, ndi dzina latsopano
la Yesu ndi Ufumu wa
Mulungu dzina la Yerusalemu
Watsopano mu m’badwo
wa Mzimu Woyera.
Kuti Tikwaniritse Tanthauzo la
Tsiku Lokwera Kumwamba, Tiyenera
Kukhala Mboni za
Mzimu ndi Mkwatibwi.
Malinga ndi mawu akuti,
“Wodala ali iye amene
asunga mawu a ulosi,”
mamembala a Mpingo wa
Mulungu amalalikira Amayi
a Kumwamba Yerusalemu
Watsopano ndi Khristu
Ahnsahnghong—Mzimu ndi
Mkwatibwi—amene abwera
monga Apulumutsi mu
m’badwo wa Mzimu Woyera.
Yesaya 43:10
“Inu ndinu mboni zanga,”
ati Yehova, “ndi mtumiki
wanga amene ndakusankha . . .”
Machitidwe 1:8
Komatu mudzalandira mphamvu,
Mzimu Woyera atadza pa
inu: ndipo mudzakhala mboni
zanga mu Yerusalemu, ndi
mu Yudeya monse, ndi
mu Samariya, ndi kufikira
malekezero ake a dziko.
Chivumbulutso 3:12
Iye wakupambana, ndidzamyesa
iye mzati wa mu Kachisi
wa Mulungu wanga, ndipo
kutuluka sadzatulukamonso; ndipo
ndidzalemba pa iye dzina
la Mulungu wanga, ndi
dzina la mzinda wa
Mulungu wanga, la Yerusalemu
watsopano, wotsika mu Mwamba,
kuchokera kwa Mulungu wanga
; ndi dzina langa latsopano.
[Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.]
〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org
〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny
〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com