Utumiki wa a Twaibu – Zokambirana za Malawi pa tsamba la chinsisi la internet la satanic pa 24 March
Living for Christ - Malawi
0:00 / 0:00
Utumiki wa a Twaibu – Zokambirana za Malawi pa tsamba la chinsisi la internet la satanic pa 24 March
8 809 просмотров · 3 года назад
Living for Christ - Malawi
11,6 тыс. подписчиков
8 809 просмотров · 3 года назад
Mu utumikiwu, a Twaibu akufotokoza zokambirana zokhudza Malawi pa tsamba la chinsisi la internet usiku wa pa 24 March 2023. Nthumwi za satanazi zikukambirana za Malawi mogwirizana ndi vuto la madzi lagwa m’dzikoli. Pa msonkhano wa kumidiwawu, palinso nduna ya dziko la Malawi yomwe ikuyankhulapo. Mverani ana a Mulungu kuti mudziwe za nthawi yomwe tikuyendayi ndi zomwe zikuchitika.