Nkhani ya Amayi | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
World Mission Society Church of God / Global
0:00 / 0:00
Nkhani ya Amayi | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
640 просмотров · 1 год назад
World Mission Society Church of God / Global
145 тыс. подписчиков
640 просмотров · 1 год назад
Amayi Akumwamba Ali ndi Yankho la Maloto a Utopian Yemwe Anthu akhala akuyang ‘ana
Baibulo limachitira umboni za Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi kudzera mwa Adamu ndi Heva.
Monga Heva amatchedwa “amayi wa amoyo onse,” anapereka moyo wakuthupi kwa anthu, ndipo Mulungu Amayi abwera padziko lapansi kudzapereka moyo wosatha kwa anthu.
Kodi Mulungu ndi Amayi, Amene Mpingo wa Mulungu Umakhulupirira, Amachitiridwa Umboni M’Baibulo?
Mulungu anati, “Tipange munthu m’chifanizo chathu, . . .” ndipo analenga mwamuna ndi mkazi, ndipo Iye anagwiritsa ntchito dzina lakuchulukitsa “Elohim” [milungu] koposa ka 2,500 m’ Baibulo.
Komanso, kuchitira umboni kuti Mulungu Amayi alipo, amene amapereka moyo wosatha kwa anthu kudzera mu chifuniro chawo cha kulenga zinthu zonse kuti zilandile moyo kokha kudzera mwa amayi.
Genesis 1: 26–27
Ndipo anati Mulungu, Tipange munthu m’chifanizo
chathu, monga mwa chikhalidwe chathu: . . .
Mulungu ndipo adalenga munthu m’chifanizo
chake, m’chifanizo cha Mulungu adamlenga iye;
adalenga iwo mwamuna ndi mkazi.
Genesis 3:20
Ndipo mwamuna anamutcha dzina la mkazi wake,
Heva; chifukwa ndiye amake wa amoyo onse.
[Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.]
〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org
〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny
〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com