Перейти к содержимому

Ndikhulupilira Bible (Official Music Video) — Area 47 Senior Youth Choir

Area 47 Senior Youth Choir

0:00 / 0:00

Ndikhulupilira Bible (Official Music Video) — Area 47 Senior Youth Choir

208 739 просмотров · 6 месяцев назад
Area 47 Senior Youth Choir
5,85 тыс. подписчиков
208 739 просмотров · 6 месяцев назад
Words & Music: Ndudirim Nwachukwu Accessed from: Tunefulness.scores Title: Oh yes, I believe ‪@tunefulness.scores‬ _________________________________________ Chichewa Lyrics: 1. Ndikhulupilira Bible, Ndukhulupilira Yesu, Kuti anafa pamtanda kufera 'ne. Ndikhulupirira Tate, Mwana ndi Mzimu Oyera, Ine, ine, ndikhulupira. Chorus Kuti anandiferane, Kuti ndikhale ndi moyo. Anafa, anafa, anafa kufera ine, Akufuna ndisiye tchimo, anafa pamtanda paja, Nagwazidwa Mbuye wanga. 2. Ndikhulupilira Yesu, Abweradi posachedwa, Kudzatenga onse kunka nawo mwamba. Kuti tikhale ndi moyo, Osatha mudziko ilo, Ine ine ndikhulupira.