LUNTHA TV || CHIDZULO || 13 OCTOBER 2026
Luntha TV official
0:00 / 0:00
LUNTHA TV || CHIDZULO || 13 OCTOBER 2026
2 837 просмотров · Трансляция закончилась 4 ч назад
Luntha TV official
29,3 тыс. подписчиков
2 837 просмотров · Трансляция закончилась 4 ч назад
LUNTHA TV || CHIDZULO: Pamene nkhani ya kusapezeka mokwanira kwa mafuta ili mkamwa mkamwa, anthu ena akuloza chala anthu ochita kabanza kuti ndi omwe akumasowetsa mafutawa akafika. Izi akuti ndi zina mwa zifukwa zomwe zikuchititsa kuti mafutawa asamakhalitse akafika pa malo ogulitsira. Komanso tikuyankhula pano ndekuti apolisi ku Lilongwe alanda zigubu zankhani nkhani Kwa anthu omwe amagulitsa mafuta mozembera boma. Nkhani imeneyi mukuimvetsa bwanji a Malawi ndipo maganizo anu ndi otani? || 13 OCTOBER 2026