Перейти к содержимому

Kukhulupirira za Umwini wa Allah | Tawuheed Islamic Education

Tawuheed Islamic Tv

0:00 / 0:00

Kukhulupirira za Umwini wa Allah | Tawuheed Islamic Education

78 просмотров · 3 нед. назад
Tawuheed Islamic Tv
78 подписчиков
78 просмотров · 3 нед. назад
Kodi kukhulupirira za umwini wa Allah (Ar-Rububiyyah) kumatanthauza chiyani m'moyo wa Mumsilimu komanso zochitika zake ndi ziti? M'kalasi yino ya Tadreebu Tullab li-Ibtidai (Sunnah Malawi), tikuphunzira mozama za chikhulupiriro ndi umwini wa Allah. 📌 M'kalasi yino muphunzira: Tanthauzo la kukhulupirira za umwini wa Allah (Ar-Rububiyyah). Zochitika zake zosiyanasiyana m'moyo wa tsiku ndi tsiku. Maphunziro a Aqeedah ophunzitsidwa m'njira yosavuta. Lumikizanani nafe pa WhatsApp: +265 982 23 83 04 (WhatsApp and call) +276 939 09242 (WhatsApp only) Chonde Like, Share ndi Subscribe pa Tawuheed Islamic TV kuti musaphonye maphunziro ena a Online Classes! #TawuheedTV #TadreebuTullab #KukhulupiriraZaUmwiniWaAllah #Aqeedah #MaphunziroAChisilamu #IslamInMalawi