Gustino - Pang'ono Ft Saint-Realest (Official Music Video)
GUSTINO
0:00 / 0:00
Gustino - Pang'ono Ft Saint-Realest (Official Music Video)
135 281 просмотр · 1 год назад
GUSTINO
4,67 тыс. подписчиков
135 281 просмотр · 1 год назад
LISTEN TO Pang'ono Here:https://onerpm.link/281101328365
@officialsaintrealest
FOLLOW GUSTINO:
Instagram: https://www.instagram.com/gustino._?igsh=M...
Twitter: https://x.com/GlProducer?t=DywRirQglcpm992...
YouTube: • Gustino-Ndidziwe (Official Music Video)
TikTok: vm.tiktok.com/ZMdxKphGu
Lyrics
Ooh oh oh
Party siyingakome popanda mabebi
(mabebi yeah)
Mowa siwungakome popanda ma chick
Iwe Bala-man mabebi onse champagne
Lero ndi party man kwayaka moto ten over ten
Sholi mama bwera undidansile undivinile pang'ono
Sholi mama bwera ndikumwazile Chikondi ndi ndalama
Mamacita senorita uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Sindinganjoye opanda njole
Ndiye mabebi adzadze lole
Thumba langali musalitole
Ndilimene likhala chikole
My pocket full of money
Fine baby sipping on wine,I mek her fi wine
She break it down properly, she say kabwerela show she don't want my love
My pocket full of money
Sindinjoya mwa lottery
Sindimaspenda mwa lottery
MaShude timaba mwa robbery
Sholi mama bwera undidansile undivinile pang'ono
Sholi mama bwera ndikumwazile Chikondi ndi ndalama
Mamacita senorita uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono
Pang'ono pang'ono uzipanga pang'ono