Saint Realest - Malesa ( Official Visualizer)
Official Saint Realest
0:00 / 0:00
Saint Realest - Malesa ( Official Visualizer)
22 678 просмотров · 11 дней назад
Official Saint Realest
93,3 тыс. подписчиков
22 678 просмотров · 11 дней назад
MALESA
{Verse 1}
Life without you be incomplete
Ngati nyimbo yopanda beat
Singakhale without you
Ine ndiri chabe without you my love
Everything is for you oh
Ndine mbalame yopanda mapiko
Nyumba yopanda denga
Am useless without you
Zoba ine without you my love
Everything is for you oh
{Chorus}
Bwanji ntchito ndileke
Ndizingogwira za iwe
Eeeh eh
Hustle ndisiye ndizithamanga za iwe
Eeh eeh eh
Honey iwe honey
Honey iwe honey
Honey iwe honey
Bwanji ntchito ndileke
Ndizingogwira za iwe
Eeeh eh
Hustle ndisiye ndizithamanga za iwe
Eeh eeh eh
Honey iwe honey
Honey iwe honey
Honey iweyo Uchi
Umakometsa moyo Malesa
{Verse 2}
Malesa baby malesa
When am with you i feel so alive
Kukuleka baby kukuleka
Ndi chimodzimodzi kuwuluza moyo
Mu mtima mwanga monsemu
Mumaganizo monsemu
Munango-loader iweyo
Oooh oh
{Chorus}
Bwanji ntchito ndileke
Ndizingogwira za iwe
Eeeh eh
Hustle ndisiye ndizithamanga za iwe
Eeh eeh eh
Honey iwe honey
Honey iwe honey
Honey iwe honey
Bwanji ntchito ndileke
Ndizingogwira za iwe
Eeeh eh
Hustle ndisiye ndizithamanga za iwe
Eeh eeh eh
Honey iwe honey
Honey iwe honey
Honey iweyo Uchi
Umakometsa moyo Malesa
{Outro}
Personal Personal
Personal human being
You’re personal personal
Personal property
You be personal personal
Personal human being
You’re my personal personal
Katundu wanga ndiwe
Property yanga ndiwe
Assert yanga ndiwe
Munthu wanga ndiwe