Перейти к содержимому

Psalmist Wanangwa Shammah ft Billy Kaunda Pafupipo final

Psalmist Wanangwa Shammah.

0:00 / 0:00

Psalmist Wanangwa Shammah ft Billy Kaunda Pafupipo final

139 807 просмотров · 5 месяцев назад
Psalmist Wanangwa Shammah.
2,48 тыс. подписчиков
139 807 просмотров · 5 месяцев назад
Moni, ndine Psalmist Wanangwa Shammah waku Lilongwe, Malawi 🙏 Mulungu wandipatsa mphatso ya nyimbo zopembedza ndi zolimbikitsa. Cholinga changa ndi kufikitsa uthenga wa chiyembekezo ndi chipulumutso kudzera mu nyimbo ngati "Pa Cavalry", "UKO", ndi "Pafupipo ndi zina zambiri" Chifukwa chiyani Patreon? Panopa YouTube monetization siyinaloledwe ku Malawi. Koma utumiki uyenera kupitilira. Thandizo lanu pa Patreon limandithandiza: 1. Kulipira studio kuti ndijambule nyimbo zatsopano 2. Kupanga ma video apamwamba a YouTube 3. Kuyenda m'ma church osiyanasiyana kukatumikira 4. Kuthandiza anthu osowa kudzera mu utumiki Mukakhala Patron wanga, simukundipatsa ndalama zokha — mukukhala gawo la utumikiwu. Tiyeni tifalitse Ufumu wa Mulungu limodzi. Kwa a ku Malawi omwe alibe khadi, mutha kutumiza chopereka chanu mwachindunji kudzera pa: 📱 Airtel Money: 0997612290 — Dzina: Wanangwa Mazunda 📱 TNM Mpamba: 0893842233 — Dzina: Wanangwa Mazunda 🏦 National Bank Account: 1014261474 — Dzina: Wanangwa Mazunda Mukatumiza, chonde nditumizireni uthenga pa WhatsApp 0997612290 kuti ndikuwonjezereni ku gulu la a Patron. Zikomo kwambiri chifukwa cha chikondi chanu. Mulungu akudalitseni. ❤️