Tiyeni Tisaiwale Lamulo la Mulungu | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
World Mission Society Church of God / Global
0:00 / 0:00
Tiyeni Tisaiwale Lamulo la Mulungu | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
359 просмотров · 5 месяцев назад
World Mission Society Church of God / Global
145 тыс. подписчиков
359 просмотров · 5 месяцев назад
N’chifukwa Chiyani Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi Anatsindika Lamulo la Mulungu?
M'moyo womvera lamulo la Mulungu, madalitso ochuluka amasungidwira ife nthaŵi zonse. Pachifukwa ichi, mkati mwa maphwando omwe Mulungu adakhazikitsa kuyambira m'badwo wa Atate—monga Sabata ndi Paska—nthawi zonse pamakhala lamulo lakuti, “Musaiwale, koma kumbukirani ndi kuwasunga kwamuyaya.”
Chifukwa Chofunika Chimene Mamembala a Mpingo wa Mulungu pa Dziko lonse Lapansi Amasunga Lamulo la Mulungu
Baibulo limati iwo amene amasunga lamulo la Mulungu m'mibadwo yonse adzadalitsidwa ngati olungama, ndipo iwo amene amaswa lamulo la Mulungu adzaweruzidwa chifukwa cha kupanduka. Aisrayeli anatengedwera ku ukapolo ku Babulo chifukwa chosasunga lamulo la Mulungu.
sitinamvere mau a Yehova Mulungu wathu, kuyenda m'malamulo ake anatiikirawo pamaso pathu, mwa atumiki ake aneneri.
Inde Israele yense walakwira chilamulo chanu, ndi kupatuka, kuti asamvere mau anu; chifukwa chake temberero lathiridwa pa ife, ndi lumbiro lolembedwa m'chilamulo cha Mose mtumiki wa Mulungu; pakuti tamchimwira.
Daniele 9:10–11
amayenda m'malemba anga, nasunga maweruzo anga kuchita chokhulupirika; iye ndiye wolungama, adzakhala ndi moyo ndithu, anena Ambuye Yehova.
Ezekiele 18:9
[Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.]
〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org
〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny
〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com