Перейти к содержимому

LUNTHA TV| CHIDZULO | 1 OCTOBER 2026

Luntha TV official

0:00 / 0:00

LUNTHA TV| CHIDZULO | 1 OCTOBER 2026

1 074 просмотра · Трансляция закончилась 12 часов назад
Luntha TV official
28,8 тыс. подписчиков
1 074 просмотра · Трансляция закончилась 12 часов назад
LUNTHA TV | CHIDZULO- Boma lasintha momwe FISP iziyendera mu 2026/27, pomwe pali zofunikira zatsopano kwa alimi, kuphatikizapo kukhala m’gulu la alimi (Farmer Organization)MK50,000 ya matumba awiri a fertilizer ndi mbeu, komanso kutenga nawo mbali pa kupanga ndi kugwiritsa ntchito Mbeya organic fertilizer.Kodi kusinthaku kukuthandiza kuti FISP ifikire alimi oyenerera bwino, kapena kukupangitsa kuti mlimi azikumana ndi zovuta zambiri kuti apeze thandizoli? || 01 OCTOBER 2026