Перейти к содержимому

M`MENE TINGATETEZERE CHUMA CHA ANA AMASIYE (KUKHALA GUARDIAN WA ANA AMASIYE)

ISLAMIC LAWS OF INHERITANCE

0:00 / 0:00

M`MENE TINGATETEZERE CHUMA CHA ANA AMASIYE (KUKHALA GUARDIAN WA ANA AMASIYE)

219 просмотров · 1 мес. назад
ISLAMIC LAWS OF INHERITANCE
46 подписчиков
219 просмотров · 1 мес. назад
Chisilamu chimalimbikitsa kwambiri kusamalira ndikuteteza chuma cha ana amasiye. Wosamalira mwana wamasiye ayenera kuteteza chuma cha mwana wamasiye ndipo asachigwiritse ntchito mopanda chillungamo. Allah walamula kuti chuma cha ana amasiye chisungidwe bwino mpaka atakula ndi kukhala okhoza kuchiyendetsa mwanzeru chuma chawo. komanso, wosamalira mwana wamasiye ayenera kuphunzitsa mwana wa masiye makhalidwe abwino, ndi mmene ngagwiritsire ntchito chuma chawo mwanzeru komanso moona mtima akadzakula. Allah atipatse tonse mtima wachifundo wosamalira ana amasiye ndi kukwaniritsa udindo umenewu mwachilungamo. AMEEN