Перейти к содержимому

ZINTHU ZOFUNIKA KULEMBA MU WILO YA CHISILAMU

ISLAMIC LAWS OF INHERITANCE

0:00 / 0:00

ZINTHU ZOFUNIKA KULEMBA MU WILO YA CHISILAMU

151 просмотр · 1 мес. назад
ISLAMIC LAWS OF INHERITANCE
46 подписчиков
151 просмотр · 1 мес. назад
Kulemba Wilo nkufunika kwambiri kwa Msilamu aliyese. Izi si nkhani ya malamulo okha, koma ndi udindo wa chipembedzo. Kulemba Wilo kumathandiza kuteteza ufulu wa anthu amene amalandila gawo lawo lachuma,kupewa mikangano ya m`banja, komaso kuonetsesta kuti chilungamo chikutsatidwa pambuyo pa imfa. Chocho,kulemba Wilo ndi njira yabwino yokonzekera tsogolo komaso ndi kuteteza banja lanu.