Mulungu Ndiye Mphamvu Yanga | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
World Mission Society Church of God / Global
0:00 / 0:00
Mulungu Ndiye Mphamvu Yanga | GUDMWM, Mpingo wa Mulungu
1 021 просмотр · 1 г. назад
World Mission Society Church of God / Global
144 тыс. подписчиков
1 021 просмотр · 1 г. назад
Mavuto Onse a Dziko Lapansi Amatibweretsera Dzowawitsa Pamene Sitidalira Mulungu
Mulungu ali ndi mphamvu yolamulira mwayi ndi tsoka la anthu onse, moyo ndi imfa, ndi kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo. Ngati ife tidalira mphamvu za dziko, chuma, ndi chidziwitso, m’malo mwa Mulungu monga mphamvu yathu, tidzawonongedwa monga mfumu ya ku Samariya inafa pokudalira mulungu wachikunja pamene iye anavulala.
Njira Yopita Kumwamba Ikhoza Kukhala Yosangalatsa Tikamavala Mphamvu ya Mulungu Wamphamvuyonse
monga momwe makolo a chikhulupiriro monga Davide, Habakuku, ndi Zekariya anagonjetsa zopinga poona Mulungu ngati mphamvu zawo ndipo nthawi zonse amadalira Mulungu muzochitika zonse, mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhala ndi moyo wachimwemwe ndi wosangalala wa chikhulupiriro, akuyenda m’njiraewu yopambana ya uthenga wabwino podalira Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Habakuku 3:18–19
(K)oma ndidzakondwera mwa Yehova, ndidzasekerera mwa Mulungu wa chipulumutso changa.
Yehova, Ambuye, ndiye mphamvu yanga, asanduliza mapazi anga ngati a mbawala, nadzandipondetsa pa misanje yanga.
[Kanema uyu ndi wotsindikizidwa ndi Gulu la Utumiki wa Dziko lapansi la Mpingo wa Mulungu. Malo osalolezedwa kapena kugawa ndi koletsedwa.]
〖World Mission Society Church of God〗https://watv.org
〖 WATV Media Cast 〗 https://watvmedia.org/ny
〖Church of God Introduction〗 https://introwmscog.com