ULALIKI WA PA NIKAH: Kuyamikirana M'banja - Abu Faruq Sheikh Chitemwe | Tawuheed Islamic TV
Tawuheed Islamic Tv
0:00 / 0:00
ULALIKI WA PA NIKAH: Kuyamikirana M'banja - Abu Faruq Sheikh Chitemwe | Tawuheed Islamic TV
69 просмотров · 2 нед. назад
Tawuheed Islamic Tv
78 подписчиков
69 просмотров · 2 нед. назад
💍 Ulaliki Wapadera wa pa Nikah!
Takulandirani ku Tawuheed Islamic TV. Mu kanemayu, tikuphunzira phunziro lofunika kwambiri lokhudza "Kuyamikirana M'banja" — momwe banja lachisilamu limayenera kumangidwa pa chikondi, ulemu, ndi kuyamikirana wina ndi mnzake.
Phunziro ili laperekedwa ndi Abu Faruq Sheikh Abdurazaq Chitemwe Swalihiyyu pa mwambo wa Nikah ku Chilambula Masjid, Salima pa 17th October 2026.
📍 Zambiri za Phunziro:
Mutu: Kuyamikirana M'banja (Ulaliki wa pa Nikah)
Wophunzitsa: Abu Faruq Sheikh Abdurazaq Chitemwe Swalihiyyu
Malo: Chilambula Masjid, Salima
Tsiku: 17th October 2026
📢 Thandizani Channel Yathu:
Kandani Subscribe kuti musaphonye mavidiyo atsopano.
Ikani Like ndi kugawana (Share) kanemayu kuti abale ndi alongo ena nawonso apindule.
Siyani ndemanga (Comment) pansipa kapena malingaliro anu.
#KuyamikiranaMbanja #UlalikiWaPaNikah #TawuheedIslamicTv #AbuFaruq #SalimaMalawi #IslamMalawi #ChitemweSwalihiyyu #dawahthroughart