SPEAKER SAMEER SULEMAN KUTOKOTA MOSASPHYATILA KU MWAMBO WA ISLAM DAWAH 2026|NDUNA ZA DPP ZISAMVE IZI
AM TV MALAWI
0:00 / 0:00
SPEAKER SAMEER SULEMAN KUTOKOTA MOSASPHYATILA KU MWAMBO WA ISLAM DAWAH 2026|NDUNA ZA DPP ZISAMVE IZI
13 930 просмотров · Трансляция закончилась 14 ч назад
AM TV MALAWI
215 тыс. подписчиков
13 930 просмотров · Трансляция закончилась 14 ч назад
Spikala wa Nyumba ya Malamulo, Sameer Suleman, wati kusowa kwa kukhulupirika kwa anthu amene apatsidwa udindo woyang’anira chuma cha boma ndi chimodzi mwa zifukwa zikulepheretsa Malawi kupita patsogolo.
Polankhula pamwambo wa Dawah 2026 womwe ukuchitika mumzinda wa Lilongwe, a Suleman watsindika kuti katangale, umbombo ndi kugwiritsa ntchito molakwika chuma cha boma zikufooketsa chitukuko cha dziko.
Iye wapempha anthu, makamaka achinyamata, kutsatira makhalidwe abwino, kufunafuna maphunziro komanso kugwiritsa ntchito ukadaulo moyenera kuti athandize pa chitukuko cha dziko. #dawah #islam #2026